Levitiko 24:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Mnyamatayo anayamba kunyoza* ndi kutukwana dzina la Mulungu.*+ Ndiye anapita naye kwa Mose.+ Dzina la mayi ake linali Selomiti, mwana wa Dibiri wa fuko la Dani. Levitiko 24:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 “Munthu wotemberera dzina la Mulungu uja, mupite naye kunja kwa msasa. Onse amene anamumva akutemberera aike manja awo pamutu pake ndipo gulu lonse limuponye miyala.+
11 Mnyamatayo anayamba kunyoza* ndi kutukwana dzina la Mulungu.*+ Ndiye anapita naye kwa Mose.+ Dzina la mayi ake linali Selomiti, mwana wa Dibiri wa fuko la Dani.
14 “Munthu wotemberera dzina la Mulungu uja, mupite naye kunja kwa msasa. Onse amene anamumva akutemberera aike manja awo pamutu pake ndipo gulu lonse limuponye miyala.+