Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Levitiko 19:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 “Uza gulu lonse la Aisiraeli kuti, ‘Mukhale oyera, chifukwa ine Yehova Mulungu wanu ndine woyera.+

  • Salimo 99:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  5 Kwezani Yehova Mulungu wathu+ ndipo mugwadireni* pachopondapo mapazi ake.+

      Iye ndi woyera.+

  • 1 Petulo 1:15, 16
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 Koma mofanana ndi Woyera amene anakuitanani, inunso khalani oyera mʼmakhalidwe anu onse,+ 16 chifukwa Malemba amati: “Mukhale oyera, chifukwa ine ndine woyera.”+

  • Chivumbulutso 4:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 8 Aliyense wa angelo 4 amenewa anali ndi mapiko 6 ndipo mapikowo anali ndi maso paliponse.+ Angelo amenewa sankapuma masana ndi usiku, ankangokhalira kunena kuti: “Woyera, woyera, woyera ndi Yehova*+ Mulungu, Wamphamvuyonse, amene analipo, amene alipo ndi amene akubwera.”+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena