Levitiko 11:44 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 44 Ine ndine Yehova Mulungu wanu.+ Mudzipatule ndi kukhala oyera,+ chifukwa ine ndine woyera.+ Choncho musamadzidetse ndi chamoyo chilichonse choyenda padziko lapansi. Levitiko 19:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 “Uza gulu lonse la Aisiraeli kuti, ‘Mukhale oyera, chifukwa ine Yehova Mulungu wanu ndine woyera.+ Levitiko 20:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Choncho mudzipatule ndipo mukhale oyera,+ chifukwa ine ndine Yehova Mulungu wanu. Levitiko 20:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Mukhale oyera kwa ine, chifukwa ine Yehova ndine woyera.+ Ine ndikukusiyanitsani ndi anthu a mitundu ina kuti mukhale anthu anga.+
44 Ine ndine Yehova Mulungu wanu.+ Mudzipatule ndi kukhala oyera,+ chifukwa ine ndine woyera.+ Choncho musamadzidetse ndi chamoyo chilichonse choyenda padziko lapansi.
26 Mukhale oyera kwa ine, chifukwa ine Yehova ndine woyera.+ Ine ndikukusiyanitsani ndi anthu a mitundu ina kuti mukhale anthu anga.+