Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Genesis 26:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 Zitatero, Isaki anayamba kudzala mbewu mʼdzikomo. Mʼchaka chimenechi anakolola zochuluka moti pa thumba limodzi lililonse la mbewu zimene anadzala anakolola matumba 100, chifukwa Yehova ankamudalitsa.+

  • Deuteronomo 28:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 8 Yehova adzadalitsa nyumba zanu zosungiramo zinthu+ komanso chilichonse chimene mukuchita ndipo adzakudalitsani mʼdziko limene Yehova Mulungu wanu akukupatsani.

  • Malaki 3:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Bweretsani gawo limodzi pa magawo 10 alionse* a zinthu zanu nʼkuziika mosungiramo zinthu zanga,+ kuti mʼnyumba mwanga mukhale chakudya.+ Ndiyeseni chonde pa nkhani imeneyi, kuti muone ngati sindidzakutsegulirani mageti akumwamba+ nʼkukukhuthulirani madalitso mpaka simudzasowa kanthu,”+ watero Yehova wa magulu ankhondo akumwamba.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena