Salimo 78:58, 59 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 58 Anapitiriza kumukhumudwitsa ndi malo awo okwezeka,+Ndipo anamukwiyitsa* ndi zifaniziro zawo zogoba.+ 59 Mulungu anamva ndipo anakwiya kwambiri,+Choncho anawakaniratu Aisiraeli.
58 Anapitiriza kumukhumudwitsa ndi malo awo okwezeka,+Ndipo anamukwiyitsa* ndi zifaniziro zawo zogoba.+ 59 Mulungu anamva ndipo anakwiya kwambiri,+Choncho anawakaniratu Aisiraeli.