Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Levitiko 25:32-34
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 32 Koma nyumba za Alevi zimene zili mʼmizinda yawo,+ Aleviwo azikhala ndi ufulu woziwombola mpaka kalekale. 33 Ndipo ngati Mlevi anagulitsa nyumba mumzinda wawo ndipo sanaiwombole, izibwezedwa kwa Mleviyo mʼChaka cha Ufulu.+ Zizikhala choncho chifukwa nyumba zamʼmizinda ya Alevi pakati pa Aisiraeli ndi za Aleviwo basi.+ 34 Komanso, asagulitse malo odyetserako ziweto+ ozungulira mizinda yawo, chifukwa amenewo ndi malo awo mpaka kalekale.

  • Yoswa 21:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Choncho Aisiraeli anamvera lamulo la Yehova nʼkupatsa Alevi mizindayo+ ndi malo ake odyetserako ziweto, kuchokera pa cholowa chawo.+

  • 2 Mbiri 11:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Aleviwo anasiya malo awo odyetserako ziweto ndi madera awo+ nʼkupita ku Yuda ndi ku Yerusalemu, chifukwa Yerobowamu ndi ana ake anachotsa Aleviwo pa udindo wokhala ansembe a Yehova.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena