Genesis 29:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Leya anakhalanso woyembekezera nʼkubereka mwana wamwamuna, ndipo anati: “Yehova wandipatsa mwana wina chifukwa wamva kudandaula kwanga kuti sindikukondedwa kwenikweni.” Choncho mwanayo anamupatsa dzina lakuti Simiyoni.*+ Genesis 46:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Ana a Simiyoni+ anali Yemueli, Yamini, Ohadi, Yakini, Zohari ndi Shauli+ mwana wa mkazi wa Chikanani. Numeri 2:12, 13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Pafupi ndi fuko limeneli pazikhala fuko la Simiyoni. Mtsogoleri wa ana a Simiyoni ndi Selumiyeli,+ mwana wa Zurisadai. 13 Asilikali ake amene analembedwa mayina alipo 59,300.+
33 Leya anakhalanso woyembekezera nʼkubereka mwana wamwamuna, ndipo anati: “Yehova wandipatsa mwana wina chifukwa wamva kudandaula kwanga kuti sindikukondedwa kwenikweni.” Choncho mwanayo anamupatsa dzina lakuti Simiyoni.*+
10 Ana a Simiyoni+ anali Yemueli, Yamini, Ohadi, Yakini, Zohari ndi Shauli+ mwana wa mkazi wa Chikanani.
12 Pafupi ndi fuko limeneli pazikhala fuko la Simiyoni. Mtsogoleri wa ana a Simiyoni ndi Selumiyeli,+ mwana wa Zurisadai. 13 Asilikali ake amene analembedwa mayina alipo 59,300.+