Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Genesis 15:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 Zimenezi zitachitika, Yehova analankhula ndi Abulamu mʼmasomphenya kuti: “Usaope+ Abulamu. Ine ndine chishango chako.+ Mphoto yako idzakhala yaikulu kwambiri.”+

  • Genesis 46:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 Ndiyeno Mulungu analankhula ndi Isiraeli mʼmasomphenya usiku kuti: “Yakobo, Yakobo!” Ndipo Yakobo anayankha kuti: “Ine mbuyanga!”

  • Ekisodo 24:9-11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 Mose, Aroni, Nadabu, Abihu ndi akulu 70 a Isiraeli anakwera mʼphirimo, 10 ndipo anaona Mulungu wa Isiraeli.+ Pansi pa mapazi ake pankaoneka ngati miyala ya safiro yoyalidwa bwino, yoyera ngati kumwamba.+ 11 Mulungu sanawononge atsogoleri a Aisiraeli,+ koma iwo anaona masomphenya a Mulungu woona ndipo anadya ndi kumwa.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena