Ekisodo 14:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Iwo anafunsa Mose kuti: “Kodi watibweretsa kuno kuti tidzafere mʼchipululu muno chifukwa chakuti mu Iguputo mulibe manda?+ Nʼchifukwa chiyani watichitira zimenezi? Nʼchifukwa chiyani watitulutsa mu Iguputo? Ekisodo 15:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Choncho anthu anayamba kungʼungʼudza motsutsana ndi Mose+ kuti: “Timwa chiyani?” Numeri 16:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Kodi ukuyesa nʼchinthu chachingʼono kuti unatichotsa mʼdziko loyenda mkaka ndi uchi kuti udzatiphere mʼchipululu muno?+ Kodi tsopano ukufunanso kuti wotilamulira ukhale iwe wekha?
11 Iwo anafunsa Mose kuti: “Kodi watibweretsa kuno kuti tidzafere mʼchipululu muno chifukwa chakuti mu Iguputo mulibe manda?+ Nʼchifukwa chiyani watichitira zimenezi? Nʼchifukwa chiyani watitulutsa mu Iguputo?
13 Kodi ukuyesa nʼchinthu chachingʼono kuti unatichotsa mʼdziko loyenda mkaka ndi uchi kuti udzatiphere mʼchipululu muno?+ Kodi tsopano ukufunanso kuti wotilamulira ukhale iwe wekha?