17 Chonde mutilole tidutse mʼdziko lanu. Sitidutsa mʼmunda wanu uliwonse, kapena mʼmunda wa mpesa uliwonse. Sitimwa madzi apachitsime chanu chilichonse. Tizingoyenda mu Msewu wa Mfumu, osakhotera kudzanja lamanja kapena lamanzere, mpaka titadutsa mʼdziko lanu.’”+