Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Numeri 23:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Kenako Balamu ananena ndakatulo yakuti:+

      “Balaki mfumu ya Mowabu wandibweretsa kuno kuchokera ku Aramu,+

      Kuchokera kumapiri akumʼmawa kuti:

      ‘Bwera, udzanditembererere Yakobo.

      Bwera, udzaitanire tsoka pa Isiraeli.’+

  • Yoswa 24:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 Kenako Balaki mwana wa Zipori, mfumu ya Mowabu, ananyamuka kukamenyana ndi Aisiraeli. Iye anaitanitsa Balamu, mwana wa Beori kuti akutemberereni.+

  • Nehemiya 13:1, 2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Pa tsiku limenelo buku la Mose linawerengedwa anthu onse akumva.+ Iwo anapeza kuti mʼbukumo analembamo kuti mbadwa iliyonse ya Amoni ndi ya Mowabu+ isamaloledwe kukhala mʼgulu la anthu a Mulungu woona,+ 2 chifukwa iwowa sanapatse Aisiraeli chakudya ndi madzi. Mʼmalomwake, analemba ganyu Balamu kuti awatemberere.+ Koma Mulungu wathu anasintha temberero limenelo kukhala dalitso.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena