Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yesaya 14:24
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 24 Yehova wa magulu ankhondo akumwamba walumbira kuti:

      “Zimene ndikufuna kuchita, zidzachitika mmene ndikufunira,

      Ndipo zimene ndasankha, ndi zimene zidzachitike.

  • Yesaya 46:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Kutatsala nthawi yaitali, ndimaneneratu zimene zidzachitike,

      Ndipo kale kwambiri ndinaneneratu zinthu zimene zidzachitike mʼtsogolo.+

      Ine ndimanena kuti, ‘Zolinga zanga zidzachitikadi,+

      Ndipo ndidzachita chilichonse chimene ndikufuna.’+

  • Mika 7:20
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 20 Yakobo mudzamusonyeza kukhulupirika.

      Abulahamu mudzamusonyeza chikondi chokhulupirika,

      Ngati mmene munalumbirira kwa makolo athu kalekale.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena