Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Salimo 96:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  5 Milungu yonse ya anthu a mitundu ina ndi milungu yopanda pake,+

      Koma Yehova ndi amene anapanga kumwamba.+

  • 1 Akorinto 10:21, 22
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 21 Sizingatheke kuti muzimwa zamʼkapu ya Yehova* komanso zamʼkapu ya ziwanda. Sizingathekenso kuti muzidya “patebulo la Yehova”*+ komanso patebulo la ziwanda. 22 Kapena ‘kodi tikufuna kuti Yehova* achite nsanje?’+ Kodi mphamvu zathu zingapose mphamvu zake?

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena