1 Samueli 2:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Yehova amapha komanso amasunga moyo,*Iye amatsitsira Kumanda* komanso amaukitsa.+ Salimo 68:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Mulungu woona ndi Mulungu amene amatipulumutsa.+Ndipo Yehova Ambuye Wamkulu Koposa amatipulumutsa ku imfa.+
20 Mulungu woona ndi Mulungu amene amatipulumutsa.+Ndipo Yehova Ambuye Wamkulu Koposa amatipulumutsa ku imfa.+