Deuteronomo 12:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Ngati mukufuna kudya nyama, mungathe kupha chiweto chanu nʼkudya nyama yake nthawi iliyonse,+ mogwirizana ndi madalitso amene Yehova Mulungu wanu wakupatsani mʼmizinda yanu yonse.* Munthu wodetsedwa komanso munthu wosadetsedwa angathe kudya nyamayo, ngati mmene mungadyere insa ndi mbawala. Deuteronomo 14:4, 5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Nyama zimene mungathe kudya+ ndi izi: ngʼombe, nkhosa, mbuzi, 5 mbawala, insa, ngondo, mbuzi yakuthengo, mphalapala, nkhosa yakuthengo ndi nkhosa yamʼmapiri.
15 Ngati mukufuna kudya nyama, mungathe kupha chiweto chanu nʼkudya nyama yake nthawi iliyonse,+ mogwirizana ndi madalitso amene Yehova Mulungu wanu wakupatsani mʼmizinda yanu yonse.* Munthu wodetsedwa komanso munthu wosadetsedwa angathe kudya nyamayo, ngati mmene mungadyere insa ndi mbawala.
4 Nyama zimene mungathe kudya+ ndi izi: ngʼombe, nkhosa, mbuzi, 5 mbawala, insa, ngondo, mbuzi yakuthengo, mphalapala, nkhosa yakuthengo ndi nkhosa yamʼmapiri.