1 Samueli 1:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 1 Panali mwamuna wina wa ku Ramatayimu-zofimu,*+ kudera lamapiri la Efuraimu,+ dzina lake Elikana.+ Iye anali mwana wa Yerohamu, mwana wa Elihu, mwana wa Tohu, mwana wa Zufi, ndipo anali wa fuko la Efuraimu.
1 Panali mwamuna wina wa ku Ramatayimu-zofimu,*+ kudera lamapiri la Efuraimu,+ dzina lake Elikana.+ Iye anali mwana wa Yerohamu, mwana wa Elihu, mwana wa Tohu, mwana wa Zufi, ndipo anali wa fuko la Efuraimu.