1 Samueli 1:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Kenako anadzuka mʼmawa ndipo atalambira Yehova anabwerera kunyumba kwawo ku Rama.+ Ndiyeno Elikana anagona ndi mkazi wake Hana ndipo Yehova anamukumbukira.+ 1 Samueli 7:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Samueli anapitiriza kuweruza Isiraeli kwa moyo wake wonse.+ 1 Samueli 7:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Akazungulirazungulira, ankabwerera ku Rama+ chifukwa nʼkumene kunali nyumba yake, ndipo kumeneko ankaweruzanso Aisiraeli. Iye anamangira Yehova guwa lansembe kumeneko.+
19 Kenako anadzuka mʼmawa ndipo atalambira Yehova anabwerera kunyumba kwawo ku Rama.+ Ndiyeno Elikana anagona ndi mkazi wake Hana ndipo Yehova anamukumbukira.+
17 Akazungulirazungulira, ankabwerera ku Rama+ chifukwa nʼkumene kunali nyumba yake, ndipo kumeneko ankaweruzanso Aisiraeli. Iye anamangira Yehova guwa lansembe kumeneko.+