1 Samueli 2:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Ana a Eli anali oipa+ ndipo sankalemekeza Yehova. 1 Samueli 2:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Pa nthawiyi Eli anali atakalamba kwambiri koma anamva zonse zimene ana ake ankachitira+ Aisiraeli onse. Anamvanso kuti ankagona ndi akazi amene ankatumikira pakhomo la chihema chokumanako.+ 1 Samueli 4:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Munthu amene anabwera ndi uthengayo anati: “Aisiraeli athawa Afilisiti, ndipo agonjetsedwa koopsa.+ Ana anunso awiri, Hofeni ndi Pinihasi, aphedwa.+ Komanso Likasa la Mulungu woona lalandidwa.”+
22 Pa nthawiyi Eli anali atakalamba kwambiri koma anamva zonse zimene ana ake ankachitira+ Aisiraeli onse. Anamvanso kuti ankagona ndi akazi amene ankatumikira pakhomo la chihema chokumanako.+
17 Munthu amene anabwera ndi uthengayo anati: “Aisiraeli athawa Afilisiti, ndipo agonjetsedwa koopsa.+ Ana anunso awiri, Hofeni ndi Pinihasi, aphedwa.+ Komanso Likasa la Mulungu woona lalandidwa.”+