Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Numeri 3:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Uike Aroni ndi ana ake kuti akhale ansembe, ndipo azigwira ntchito zawo zaunsembe.+ Munthu wamba* aliyense amene wayandikira malowo, aziphedwa.”+

  • Deuteronomo 33:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Amenewa azilangiza Yakobo pa zigamulo zanu+

      Ndi Isiraeli mʼChilamulo chanu.+

      Azipereka nsembe zofukiza kuti zikhale kafungo kosangalatsa kwa inu,*+

      Ndi nsembe yathunthu paguwa lanu lansembe.+

  • Malaki 2:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Wansembe ayenera kuphunzitsa anthu za Mulungu. Anthu ayenera kupita kwa iye kuti akamve Chilamulo*+ chifukwa iye ndi mthenga wa Yehova wa magulu ankhondo akumwamba.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena