1 Samueli 19:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Davide anathawa nʼkukafika kwa Samueli ku Rama+ ndipo anafotokozera Samueli zonse zimene Sauli anamuchitira. Kenako Davide ndi Samueli anachoka nʼkukakhala ku Nayoti.+
18 Davide anathawa nʼkukafika kwa Samueli ku Rama+ ndipo anafotokozera Samueli zonse zimene Sauli anamuchitira. Kenako Davide ndi Samueli anachoka nʼkukakhala ku Nayoti.+