1 Samueli 7:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Samueli anapitiriza kuweruza Isiraeli kwa moyo wake wonse.+ 1 Samueli 7:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Akazungulirazungulira, ankabwerera ku Rama+ chifukwa nʼkumene kunali nyumba yake, ndipo kumeneko ankaweruzanso Aisiraeli. Iye anamangira Yehova guwa lansembe kumeneko.+
17 Akazungulirazungulira, ankabwerera ku Rama+ chifukwa nʼkumene kunali nyumba yake, ndipo kumeneko ankaweruzanso Aisiraeli. Iye anamangira Yehova guwa lansembe kumeneko.+