Levitiko 7:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Nyama ya nsembe zamgwirizano zimene zaperekedwa monga nsembe yoyamikira aziidya pa tsiku limene waipereka. Asasunge nyama iliyonse mpaka mʼmamawa.+
15 Nyama ya nsembe zamgwirizano zimene zaperekedwa monga nsembe yoyamikira aziidya pa tsiku limene waipereka. Asasunge nyama iliyonse mpaka mʼmamawa.+