Salimo 37:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Ndinali mwana ndipo tsopano ndakula,Koma sindinaonepo munthu aliyense wolungama atasiyidwa,+Kapena ana ake akupemphapempha chakudya.+ Mateyu 6:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Mutipatse chakudya chimene* tikufunikira lero.+
25 Ndinali mwana ndipo tsopano ndakula,Koma sindinaonepo munthu aliyense wolungama atasiyidwa,+Kapena ana ake akupemphapempha chakudya.+