Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 1 Mafumu 18:23, 24
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 23 Iwowo apeze ngʼombe zamphongo ziwiri zingʼonozingʼono. Asankhepo ngʼombe imodzi nʼkuiduladula. Ndiyeno aiike pankhuni koma asayatsepo moto. Ineyo ndikonza ngʼombe inayo nʼkuiika pankhuni, ndipo nanenso sindiyatsapo moto. 24 Kenako muitane dzina la mulungu wanu.+ Inenso ndiitana dzina la Yehova, ndipo Mulungu amene ayankhe potumiza moto asonyeza kuti ndi Mulungu woona.”+ Anthu onsewo atamva zimenezi anayankha kuti: “Zili bwino.”

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena