Ekisodo 3:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Mose anakhala mʼbusa wa ziweto za Yetero*+ apongozi ake, wansembe wa ku Midiyani. Pamene ankaweta ziwetozo chakumadzulo kwa chipululu, anafika kuphiri la Mulungu woona, ku Horebe.+ Ekisodo 19:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Phiri la Sinai linafuka utsi paliponse, chifukwa chakuti Yehova anabwera paphiripo mʼmoto.+ Utsi wakewo unkakwera kumwamba ngati utsi wa uvuni ndipo phiri lonse linkanjenjemera kwambiri.+ Malaki 4:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 “Kumbukirani Chilamulo cha Mose mtumiki wanga. Kumbukirani malamulo ndi ziweruzo zomwe ndinamupatsa ku Horebe kuti Aisiraeli onse azitsatira.+
3 Mose anakhala mʼbusa wa ziweto za Yetero*+ apongozi ake, wansembe wa ku Midiyani. Pamene ankaweta ziwetozo chakumadzulo kwa chipululu, anafika kuphiri la Mulungu woona, ku Horebe.+
18 Phiri la Sinai linafuka utsi paliponse, chifukwa chakuti Yehova anabwera paphiripo mʼmoto.+ Utsi wakewo unkakwera kumwamba ngati utsi wa uvuni ndipo phiri lonse linkanjenjemera kwambiri.+
4 “Kumbukirani Chilamulo cha Mose mtumiki wanga. Kumbukirani malamulo ndi ziweruzo zomwe ndinamupatsa ku Horebe kuti Aisiraeli onse azitsatira.+