Machitidwe 7:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Anamupatsanso pangano la mdulidwe.+ Kenako anabereka Isaki+ ndipo anamudula pa tsiku la 8.+ Nayenso Isaki anabereka* Yakobo ndipo Yakobo anabereka mitu ya mabanja 12 ija.
8 Anamupatsanso pangano la mdulidwe.+ Kenako anabereka Isaki+ ndipo anamudula pa tsiku la 8.+ Nayenso Isaki anabereka* Yakobo ndipo Yakobo anabereka mitu ya mabanja 12 ija.