Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Levitiko 26:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 Ine ndidzakukanani, ndipo adani anu adzakugonjetsani+ ndi kukuponderezani,+ moti muzidzathawa popanda munthu wokuthamangitsani.+

  • Levitiko 26:37
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 37 Iwo adzagwetsana okhaokha ngati anthu amene akuthawa lupanga, koma popanda munthu wowathamangitsa. Simudzatha nʼkomwe kulimbana ndi adani anu.+

  • Deuteronomo 32:30
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 30 Kodi munthu mmodzi angathamangitse bwanji anthu 1,000,

      Kapena anthu awiri angathamangitse bwanji anthu 10,000?+

      Nʼzosatheka, pokhapokha Thanthwe lawo litawagulitsa,+

      Komanso ngati Yehova atawapereka.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena