Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Nehemiya 13:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Mundikumbukire,+ inu Mulungu wanga, chifukwa cha zinthu zimenezi ndiponso chikondi chokhulupirika chimene ndinasonyeza chifukwa cha nyumba ya Mulungu wanga ndi zonse zochitika kumeneko.+

  • Salimo 18:24
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 24 Yehova andipatse mphoto chifukwa choti ndine wolungama,+

      Komanso chifukwa choti ndine wosalakwa pamaso pake.+

  • Yesaya 38:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 “Yehova ndikukupemphani kuti chonde, mukumbukire+ kuti ndinayenda pamaso panu mokhulupirika ndiponso ndi mtima wonse+ komanso ndachita zabwino pamaso panu.” Kenako Hezekiya anayamba kulira kwambiri.

  • Malaki 3:16
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 16 Pa nthawi imeneyo anthu oopa Yehova ankalankhulana, aliyense ndi mnzake, ndipo Yehova anatchera khutu nʼkumamvetsera. Buku la chikumbutso, lonena za anthu oopa Yehova ndi anthu amene ankaganizira za dzina lake,* linayamba kulembedwa pamaso pake.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena