Ezara 1:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Koresi mfumu ya Perisiya anatuma msungichuma Mitiredati kuti abweretse ziwiyazo nʼkuziwerenga. Atatero anazipereka kwa Sezibazara*+ mtsogoleri wa Yuda. Ezara 1:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Ziwiya zonse zagolide ndi zasiliva zinalipo 5,400. Sezibazara anatenga zinthu zonsezi pamene anthu amene anagwidwa ukapolo+ ankachoka ku Babulo kupita ku Yerusalemu. Zekariya 4:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 “Manja a Zerubabele anayala maziko a nyumbayi+ ndipo manja ake omwewo adzaimalizitsa.+ Ndipo mudzadziwa kuti Yehova wa magulu ankhondo akumwamba wandituma kwa inu. Mateyu 1:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Ayuda atatengedwa kupita ku Babulo, Yekoniya anabereka Salatiyeli.Salatiyeli anabereka Zerubabele.+
8 Koresi mfumu ya Perisiya anatuma msungichuma Mitiredati kuti abweretse ziwiyazo nʼkuziwerenga. Atatero anazipereka kwa Sezibazara*+ mtsogoleri wa Yuda.
11 Ziwiya zonse zagolide ndi zasiliva zinalipo 5,400. Sezibazara anatenga zinthu zonsezi pamene anthu amene anagwidwa ukapolo+ ankachoka ku Babulo kupita ku Yerusalemu.
9 “Manja a Zerubabele anayala maziko a nyumbayi+ ndipo manja ake omwewo adzaimalizitsa.+ Ndipo mudzadziwa kuti Yehova wa magulu ankhondo akumwamba wandituma kwa inu.
12 Ayuda atatengedwa kupita ku Babulo, Yekoniya anabereka Salatiyeli.Salatiyeli anabereka Zerubabele.+