Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Genesis 3:19
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 19 Udzadya chakudya kuchokera mʼthukuta la nkhope yako mpaka utabwerera kunthaka, chifukwa nʼkumene unatengedwa.+ Popeza ndiwe fumbi, kufumbiko udzabwerera.”+

  • Genesis 47:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 Yakobo anayankha Farao kuti: “Ndili ndi zaka 130 ndipo pa zaka zimenezi ndakhala ndikuyendayenda* mʼmalo osiyanasiyana. Ndakhala ndi moyo zaka zowerengeka komanso zosautsa,+ ndipo si zambiri poyerekezera ndi zaka zimene makolo anga akhala akuyendayenda mʼmalo osiyanasiyana.”+

  • Salimo 90:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Masiku a moyo wathu amangokwana zaka 70

      Kapena 80+ ngati munthu ali ndi mphamvu zambiri.*

      Koma zimakhala zodzaza ndi mavuto komanso chisoni.

      Zimatha mofulumira ndipo moyo wathu umachoka.+

  • Mlaliki 2:23
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 23 Chifukwa masiku onse a moyo wake, ntchito yakeyo imamubweretsera zowawa ndi zokhumudwitsa.+ Ndipo ngakhale usiku mtima wake supuma.+ Izinso nʼzachabechabe.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena