Yobu 14:1, 2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 “Munthu wobadwa kwa mkazi,Amakhala ndi moyo waufupi+ komanso wodzaza ndi mavuto.+ 2 Amaphuka ngati duwa kenako nʼkufota.+Amathawa ngati mthunzi ndipo saonekanso.+ Luka 12:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Choncho siyani kudera nkhawa kuti mudzadya chiyani komanso kuti mudzamwa chiyani ndipo siyani kuvutika mumtima.+
14 “Munthu wobadwa kwa mkazi,Amakhala ndi moyo waufupi+ komanso wodzaza ndi mavuto.+ 2 Amaphuka ngati duwa kenako nʼkufota.+Amathawa ngati mthunzi ndipo saonekanso.+
29 Choncho siyani kudera nkhawa kuti mudzadya chiyani komanso kuti mudzamwa chiyani ndipo siyani kuvutika mumtima.+