Salimo 37:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Kwatsala kanthawi kochepa, ndipo oipa sadzakhalaponso.+Udzayangʼana pamene ankakhala,Ndipo sadzapezekapo.+ Salimo 92:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Anthu oipa akaphuka ngati msipuNdipo anthu onse ochita zoipa zinthu zikamawayendera bwino,Zimatero kuti awonongedwe kwamuyaya.+ Yakobo 1:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Dzuwa likatuluka limatentha kwambiri nʼkufotetsa zomera ndipo maluwa a zomerazo amathothoka moti kukongola kwake kumatha. Mofanana ndi zimenezi munthu wachumayo adzafa ali mkati mofunafuna chuma.+
10 Kwatsala kanthawi kochepa, ndipo oipa sadzakhalaponso.+Udzayangʼana pamene ankakhala,Ndipo sadzapezekapo.+
7 Anthu oipa akaphuka ngati msipuNdipo anthu onse ochita zoipa zinthu zikamawayendera bwino,Zimatero kuti awonongedwe kwamuyaya.+
11 Dzuwa likatuluka limatentha kwambiri nʼkufotetsa zomera ndipo maluwa a zomerazo amathothoka moti kukongola kwake kumatha. Mofanana ndi zimenezi munthu wachumayo adzafa ali mkati mofunafuna chuma.+