Rute 4:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Zitatero, Boazi anapita kugeti la mzinda+ nʼkukhala pansi. Ali kumeneko anaona wowombola anamutchula uja+ akudutsa. Ndiyeno Boazi anati: “Iwe uje, tabwera udzakhale apa.” Choncho anapita nʼkukakhala pansi. Miyambo 31:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Mwamuna wake amadziwika bwino pamageti a mzinda,+Pamene amakhala pamodzi ndi akulu amʼdzikolo.
4 Zitatero, Boazi anapita kugeti la mzinda+ nʼkukhala pansi. Ali kumeneko anaona wowombola anamutchula uja+ akudutsa. Ndiyeno Boazi anati: “Iwe uje, tabwera udzakhale apa.” Choncho anapita nʼkukakhala pansi.