Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Rute 4:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 Zitatero, Boazi anapita kugeti la mzinda+ nʼkukhala pansi. Ali kumeneko anaona wowombola anamutchula uja+ akudutsa. Ndiyeno Boazi anati: “Iwe uje, tabwera udzakhale apa.” Choncho anapita nʼkukakhala pansi.

  • Yobu 29:7, 8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  7 Pa nthawi imene ndinkakonda kupita pageti la mzinda+

      Nʼkukakhala pabwalo la mzinda,+

       8 Anyamata ankandiona nʼkupatuka,*

      Ndipo ngakhale achikulire ankaimirira pondipatsa ulemu.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena