Genesis 31:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Koma usiku mʼmaloto,+ Mulungu anafikira Labani wa Chiaramuyo+ nʼkumuuza kuti: “Usamale ndi zimene ukalankhule ndi Yakobo, kaya zabwino kapena zoipa.”+
24 Koma usiku mʼmaloto,+ Mulungu anafikira Labani wa Chiaramuyo+ nʼkumuuza kuti: “Usamale ndi zimene ukalankhule ndi Yakobo, kaya zabwino kapena zoipa.”+