Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Nehemiya 9:33
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 33 Inu mwachita zinthu molungama pa zonse zimene zatichitikira. Mwachita zinthu mokhulupirika koma ife ndi amene tachita zinthu zoipa.+

  • Salimo 35:28
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 28 Ndipo lilime langa lidzafotokoza* za chilungamo chanu,+

      Komanso kukutamandani tsiku lonse.+

  • Salimo 59:16
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 16 Koma ine, ndidzaimba za mphamvu zanu.+

      Mʼmawa ndidzanena mosangalala za chikondi chanu chokhulupirika.

      Chifukwa inu ndinu malo anga othawirako otetezeka,+

      Ndiponso malo anga othawirako pa nthawi ya mavuto.+

  • Danieli 9:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Inu Yehova ndinu wolungama, koma ifeyo tadzibweretsera manyazi* ngati mmene zilili lero. Manyazi agwira amuna a mu Yuda, anthu a ku Yerusalemu ndi anthu onse a ku Isiraeli, amene ali pafupi ndiponso amene ali kutali, kumayiko onse amene munawabalalitsirako chifukwa choti anakuchitirani zinthu zosakhulupirika.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena