Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yobu 37:23
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 23 Wamphamvuyonse sitingathe kumumvetsa.+

      Iye ali ndi mphamvu zazikulu,+

      Ndipo sachita zinthu zosemphana ndi chilungamo+ chake komanso kulungama kwake kodabwitsa.+

  • Salimo 21:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Nyamukani, inu Yehova, muonetse mphamvu zanu.

      Tidzaimba nyimbo zotamanda mphamvu zanu.

  • Salimo 145:10-12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Ntchito zanu zonse zidzakutamandani, inu Yehova,+

      Ndipo okhulupirika anu adzakutamandani.+

      כ [Kaph]

      11 Iwo adzalengeza za ulemerero wa ufumu wanu+

      Komanso adzalankhula za mphamvu zanu,+

      ל [Lamed]

      12 Kuti anthu adziwe za ntchito zanu zamphamvu+

      Ndiponso kukula kwa ulemerero wa ufumu wanu.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena