Salimo 50:13-15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Kodi ndiyenera kudya nyama ya ngʼombe zamphongoKapena kumwa magazi a mbuzi?+ 14 Yamikani Mulungu kuti ikhale ngati nsembe imene mukupereka kwa iye,+Ndipo perekani kwa Wamʼmwambamwamba zimene mwalonjeza.+15 Pa nthawi yamavuto mundiitane.+ Ine ndidzakupulumutsani, ndipo inu mudzandilemekeza.”+ Hoseya 14:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Bwererani kwa Yehova ndi mawu amenewa.Uzani Mulungu kuti, ‘Tikhululukireni zolakwa zathu.+ Landirani zinthu zathu zabwino,Ndipo tidzakutamandani ndi pakamwa pathu+ ngati mmene tingaperekere nsembe kwa inu ana a ngʼombe amphongo.
13 Kodi ndiyenera kudya nyama ya ngʼombe zamphongoKapena kumwa magazi a mbuzi?+ 14 Yamikani Mulungu kuti ikhale ngati nsembe imene mukupereka kwa iye,+Ndipo perekani kwa Wamʼmwambamwamba zimene mwalonjeza.+15 Pa nthawi yamavuto mundiitane.+ Ine ndidzakupulumutsani, ndipo inu mudzandilemekeza.”+
2 Bwererani kwa Yehova ndi mawu amenewa.Uzani Mulungu kuti, ‘Tikhululukireni zolakwa zathu.+ Landirani zinthu zathu zabwino,Ndipo tidzakutamandani ndi pakamwa pathu+ ngati mmene tingaperekere nsembe kwa inu ana a ngʼombe amphongo.