Salimo 37:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Kwatsala kanthawi kochepa, ndipo oipa sadzakhalaponso.+Udzayangʼana pamene ankakhala,Ndipo sadzapezekapo.+ Salimo 37:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Koma oipa onse adzatheratu,+Adani a Yehova adzasowa mofulumira ngati malo okongola odyetsera ziweto amene msipu wake wobiriwira suchedwa kufota.Iwo adzatha mofulumira ngati utsi. Salimo 55:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Koma inu Mulungu, mudzatsitsira oipawo mʼdzenje lakuya.+ Anthu amene ali ndi mlandu wa magazi komanso achinyengowo, sadzakwanitsa kukhala ngakhale hafu ya moyo wawo.+ Koma ine ndidzakhulupirira inu. Miyambo 3:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Yehova amatemberera banja la munthu woipa,+Koma iye amadalitsa nyumba ya munthu wolungama.+
10 Kwatsala kanthawi kochepa, ndipo oipa sadzakhalaponso.+Udzayangʼana pamene ankakhala,Ndipo sadzapezekapo.+
20 Koma oipa onse adzatheratu,+Adani a Yehova adzasowa mofulumira ngati malo okongola odyetsera ziweto amene msipu wake wobiriwira suchedwa kufota.Iwo adzatha mofulumira ngati utsi.
23 Koma inu Mulungu, mudzatsitsira oipawo mʼdzenje lakuya.+ Anthu amene ali ndi mlandu wa magazi komanso achinyengowo, sadzakwanitsa kukhala ngakhale hafu ya moyo wawo.+ Koma ine ndidzakhulupirira inu.