Mlaliki 12:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Poti zonse zanenedwa, mfundo yaikulu ndi yakuti: Opa Mulungu woona+ ndi kusunga malamulo ake+ chifukwa zimenezi ndi zimene munthu akuyenera kuchita.+ Yeremiya 32:39 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 39 Ndidzawapatsa mtima umodzi+ komanso kuwachititsa kuti aziyenda mʼnjira imodzi kuti azindiopa nthawi zonse. Ndidzachita zimenezi kuti iwo limodzi ndi ana awo zinthu ziziwayendera bwino.+
13 Poti zonse zanenedwa, mfundo yaikulu ndi yakuti: Opa Mulungu woona+ ndi kusunga malamulo ake+ chifukwa zimenezi ndi zimene munthu akuyenera kuchita.+
39 Ndidzawapatsa mtima umodzi+ komanso kuwachititsa kuti aziyenda mʼnjira imodzi kuti azindiopa nthawi zonse. Ndidzachita zimenezi kuti iwo limodzi ndi ana awo zinthu ziziwayendera bwino.+