Yobu 28:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Ndiyeno anauza munthu kuti: ‘Tamvera, kuopa Yehova ndi nzeru,+Ndipo kupewa zoipa ndiko kumvetsa zinthu.’”+ Salimo 111:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Chiyambi cha nzeru ndi kuopa Yehova.+ ש [Sin] Onse otsatira malamulo ake amasonyeza kuti ndi ozindikira.+ ת [Taw] Iye ayenera kutamandidwa mpaka kalekale. Miyambo 1:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Kuopa Yehova ndi chiyambi cha kudziwa zinthu.+ Zitsiru zokha ndi zimene zimanyoza nzeru komanso malangizo.+
28 Ndiyeno anauza munthu kuti: ‘Tamvera, kuopa Yehova ndi nzeru,+Ndipo kupewa zoipa ndiko kumvetsa zinthu.’”+
10 Chiyambi cha nzeru ndi kuopa Yehova.+ ש [Sin] Onse otsatira malamulo ake amasonyeza kuti ndi ozindikira.+ ת [Taw] Iye ayenera kutamandidwa mpaka kalekale.
7 Kuopa Yehova ndi chiyambi cha kudziwa zinthu.+ Zitsiru zokha ndi zimene zimanyoza nzeru komanso malangizo.+