Yesaya 63:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Pamene iwo anali kuvutika m’masautso awo onse, iyenso anali kuvutika.+ Mthenga amene iye anawatumizira, anawapulumutsa.+ Chifukwa cha chikondi chake ndi chisoni chake, iye anawawombola.+ Anawakweza m’mwamba ndi kuwanyamula masiku onse akale.+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 63:9 Kuyankha Mafunso a M’Baibulo, Nsanja ya Olonda (Yogawira),No. 3 2018, tsa. 8 Yesaya 2, ptsa. 354-356
9 Pamene iwo anali kuvutika m’masautso awo onse, iyenso anali kuvutika.+ Mthenga amene iye anawatumizira, anawapulumutsa.+ Chifukwa cha chikondi chake ndi chisoni chake, iye anawawombola.+ Anawakweza m’mwamba ndi kuwanyamula masiku onse akale.+
63:9 Kuyankha Mafunso a M’Baibulo, Nsanja ya Olonda (Yogawira),No. 3 2018, tsa. 8 Yesaya 2, ptsa. 354-356