Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Levitiko 19:16
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 16 Usamayendeyende pakati pa anthu a mtundu wako nʼkumafalitsa miseche.+ Usachite kanthu kalikonse kuti uphetse mnzako.*+ Ine ndine Yehova.

  • Salimo 101:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  5 Aliyense wonenera mnzake miseche,+

      Ndidzamukhalitsa chete.*

      Aliyense amene ali ndi mtima wonyada komanso wodzikweza,

      Sindidzamulekerera.

  • Miyambo 20:19
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 19 Wonenera anzake zoipa amayendayenda nʼkumaulula zinsinsi.+

      Usamagwirizane ndi munthu amene amakonda kunena miseche.*

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena