Salimo 15:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Inu Yehova, ndi ndani amene angakhale mlendo mutenti yanu? Ndi ndani amene angakhale mʼphiri lanu lopatulika?+ Salimo 15:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Iye sanena miseche ndi lilime lake,+Sachitira mnzake choipa chilichonse,+Ndipo sanyoza* anzake.+
15 Inu Yehova, ndi ndani amene angakhale mlendo mutenti yanu? Ndi ndani amene angakhale mʼphiri lanu lopatulika?+