Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Salimo 119:33
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 33 Ndiphunzitseni inu Yehova,+ kuti ndizichita zinthu mogwirizana ndi malangizo anu,

      Ndipo ndidzawatsatira kwa moyo wanga wonse.+

  • Yesaya 30:20
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 20 Ngakhale kuti Yehova adzakupatsani mavuto kuti akhale chakudya chanu ndi kuponderezedwa kuti kukhale madzi anu akumwa,+ Mlangizi wanu wamkulu adzasiya kudzibisa ndipo maso anu adzaona Mlangizi wanu wamkulu.+

  • Mika 4:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  2 Anthu ochokera mʼmitundu yosiyanasiyana adzabwera nʼkunena kuti:

      “Bwerani, tiyeni tipite kuphiri la Yehova,

      Tipite kunyumba ya Mulungu wa Yakobo.+

      Iye akatiphunzitsa njira zake,

      Ndipo ife tidzayenda mʼnjira zakezo.”

      Chifukwa chilamulo,* chidzaphunzitsidwa mu Ziyoni

      Ndipo mawu a Yehova adzaphunzitsidwa mu Yerusalemu.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena