Salimo 37:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Chifukwa Yehova amakonda chilungamo,Ndipo sadzasiya anthu ake okhulupirika.+ ע [Ayin] Adzawateteza nthawi zonse.+Koma mbadwa za anthu oipa zidzaphedwa.+ Salimo 145:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Yehova amayangʼanira onse amene amamukonda,+Koma oipa onse adzawawononga.+
28 Chifukwa Yehova amakonda chilungamo,Ndipo sadzasiya anthu ake okhulupirika.+ ע [Ayin] Adzawateteza nthawi zonse.+Koma mbadwa za anthu oipa zidzaphedwa.+