Salimo 97:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Inu amene mumakonda Yehova, muzidana ndi zoipa.+ Iye amateteza moyo wa anthu ake okhulupirika.+Amawapulumutsa mʼmanja mwa* oipa.+ Miyambo 2:7, 8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Anthu owongoka mtima, amawasungira nzeru zopindulitsa.Iye ndi chishango kwa anthu amene amachita zinthu mokhulupirika.+ 8 Amayangʼanira njira za anthu amene amachita zachilungamo,Ndipo adzateteza njira ya anthu ake okhulupirika.+
10 Inu amene mumakonda Yehova, muzidana ndi zoipa.+ Iye amateteza moyo wa anthu ake okhulupirika.+Amawapulumutsa mʼmanja mwa* oipa.+
7 Anthu owongoka mtima, amawasungira nzeru zopindulitsa.Iye ndi chishango kwa anthu amene amachita zinthu mokhulupirika.+ 8 Amayangʼanira njira za anthu amene amachita zachilungamo,Ndipo adzateteza njira ya anthu ake okhulupirika.+