Salimo 31:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Kondani Yehova, inu nonse amene muli okhulupirika kwa iye!+ Yehova amateteza okhulupirika,+Koma aliyense wodzikuza amamulanga kwambiri.+ Salimo 97:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Inu amene mumakonda Yehova, muzidana ndi zoipa.+ Iye amateteza moyo wa anthu ake okhulupirika.+Amawapulumutsa mʼmanja mwa* oipa.+
23 Kondani Yehova, inu nonse amene muli okhulupirika kwa iye!+ Yehova amateteza okhulupirika,+Koma aliyense wodzikuza amamulanga kwambiri.+
10 Inu amene mumakonda Yehova, muzidana ndi zoipa.+ Iye amateteza moyo wa anthu ake okhulupirika.+Amawapulumutsa mʼmanja mwa* oipa.+