Salimo 33:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Muimbireni nyimbo yatsopano.+Imbani mwaluso choimbira cha zingwe ndipo muzifuula mosangalala. Salimo 96:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 96 Imbirani Yehova nyimbo yatsopano.+ Dziko lonse lapansi liimbire Yehova.+ Salimo 149:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 149 Tamandani Ya!* Imbirani Yehova nyimbo yatsopano,+Mutamandeni mumpingo wa anthu ake okhulupirika.+ Yesaya 42:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Imbirani Yehova nyimbo yatsopano.+Mʼtamandeni kuchokera kumalekezero a dziko lapansi,+Inu nonse amene mumadalira nyanja komanso zonse zimene zimakhala mmenemo,Inu zilumba ndi anthu amene amakhala mʼzilumbazo.+
149 Tamandani Ya!* Imbirani Yehova nyimbo yatsopano,+Mutamandeni mumpingo wa anthu ake okhulupirika.+
10 Imbirani Yehova nyimbo yatsopano.+Mʼtamandeni kuchokera kumalekezero a dziko lapansi,+Inu nonse amene mumadalira nyanja komanso zonse zimene zimakhala mmenemo,Inu zilumba ndi anthu amene amakhala mʼzilumbazo.+