Salimo 149:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Isiraeli asangalale ndi Mlengi wake Wamkulu.+Ana a Ziyoni akondwere ndi Mfumu yawo.